Mbili Yakale komanso Baibo
Baibo ni buku lapadela kwambili tikaganizila zimene zinacitika kuti isungidwe kwa nthawi yaitali, imasulilidwe komanso kufalitsidwa. Zimene akatswili apeza posacedwapa zikupitilizabe kutsimikizila kuti ni yolondola. Kaya muli m’cipembedzo canji, nanunso mungavomeleze kuti Baibo siingalingane na buku ina iliyonse.
KUYANKHA MAFUNSO A M’BAIBO
Kodi Baibo Anaisintha Kapena Anangoisinthako Zina?
Popeza kuti Baibo ni buku lakale kwambili, kodi tingatsimikize bwanji kuti uthenga umene ulimo wakhala ukutetezedwa kuti ukhale wolondola?