N’ciani Catsopano?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Zinthu Zocititsa Cidwi Zochulidwa m’Baibo—Maukonde Ogwilila Nsomba a m’Nthawi za m’Baibo
Dziwani zambili zokhudza maukonde ogwilila nsomba ochulidwa m’Baibo.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mafunso Ocokela Kwa Owelenga—June 2026
Malinga ndi Agalatiya 4:24, kodi zipangano ziwili zimene mtumwi Paulo anakamba zikuimila ciani?
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Gustavo Joseph: Ndatumikila Yehova kwa Zaka Pafupi-fupi 70 ku Cuba
M’bale Gustavo Joseph afotokoza mmene umoyo unalili kwa iye ndi mkazi wake pamene anali kutumikila m’dela, kulela ana, komanso pamene anaitanidwa kukatumikila pa Beteli.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
June 2026
Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila kuyambila August 10–September 6, 2026.
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
N’dzayembekezela Yehova
Ngati tatsekeledwa m’ndende, tiziyembekezela Yehova mwa kuganizila zinthu zina osati mabvuto amene tikukumana nao ndi kuyesetsa kumalimbitsa cikhulupililo cathu.

