Nyuzi
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu Ciunikilo cino, tiona kufunika kowaona moyenela abale ndi alongo amene amaonekela m’mavidiyo athu.
NKHANI ZATSOPANO
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu Ciunikilo cino, tiona kufunika kowaona moyenela abale ndi alongo amene amaonekela m’mavidiyo athu.
Ciunikilo Na 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2024.
Mu Ciunikilo cino, tiimve mmene zinthu zilili kwa abale ndi alongo athu m’maiko osiyanasiyana. Kuonjezela apo, tikhalenso ndi mwayi wokambilana ndi abale awili, m’bale Jody Jedele ndi m’bale Jacob Rumph amene ndi mamembala atsopano a Bungwe lolamulila.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
M’ciunikilo cino, tione zimene tingacite kuti tipitilize kuyambitsa maphunzilo a Baibulo.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tiphunzile zimene zingatithandize kuti tiziika maganizo athu pa Ufumu wa Mulungu omwe ndiwo yankho lokha la mavuto amene timakumana nawo.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tiona mmene abale na alongo amene ali mundende cifukwa ca cikhulupililo cawo ‘akugonjetsela coipa mwa kucita cabwino.’—Aroma 12:21.
Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tikambilana mfundo za m’Baibo zimene zingatithandize kupanga zisankho pa nkhani ya kavalidwe na kudzikongoletsa.
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Mu ciunikilo cino, tione mmene Atate wathu Yehova amaonetsela kuti “akufuna kuti anthu onse alape.” (2 Pet. 3:9 Tionenso masinthidwe amene apangidwa pa nkhani ya mavalidwe athu pamene tili ku misonkhano ya mpingo kapena ikulu-ikulu.
Ciunikilo Na. 1 ca Bungwe Lolamulila mu 2024
Onani mmene kukonda anthu kumatithandizila kukhala okangalika mu utumiki.
Ciunikilo Na. 8 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Dziŵani mmene timaonetsela kuti ndife atumiki a Mulungu pa zisankho zathu pa nkhani ya kavalidwe na kudzikongoletsa. Komanso onani zimene mungacite kuti musungitse mtendele mu mpingo.
Ciunikilo Na. 7 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Imvani za buku latsopano lakuti Malemba Othandiza pa Umoyo Wathu wa Cikhristu komanso lemba la caka ca 2024.
Ciunikilo Na. 6 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Mu ciunikilo cino, wa m’Bungwe Lolamulila agaŵana nafe nkhani yolimbikitsa ya Negede Teklemariam.
Ciunikilo Na. 5 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Mu ciunikilo cino, wa m’Bungwe Lolamulila aonetsa vidiyo yolimbikitsa ya Dennis Christensen na mkazi wake Irina.
Ciunikilo Na. 4 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Mu lipoti lino, wa m’Bungwe Lolamulila atithandiza kuyembekezela mwacidwi misonkhano yacigawo ya pamasompamaso komanso afotokoza mmene Yehova amatetezela anthu ake mwauzimu.
Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
M’bale wa m’Bungwe lolamulila ationetsa mmene abale na alongo athu akupangila Yehova kukhala pothaŵilapo pawo mosasamala kanthu za mavuto aakulu amene akukumana nawo.
Ciunikilo Na. 2 ca Bungwe Lolamulila mu 2023
Mu lipoti lino, wa m’Bungwe Lolamulila atiunikila mmene zinthu zilili kwa abale athu ku Türkiye komanso muli mbali yolimbikitsa yofunsa mafunso.