Nkhani Zaposacedwa Zimene Zinaonekela pa Tsamba Loyamba
Kodi Mulungu Amawaganizila Akazi?
Yankho la funsoli lingakuthandizeni kupeza mtendele mukamacitilidwa nkhanza kapena zinthu zina zopanda cilungamo cifukwa coti ndinu mkazi.
Mafunso 5 Pankhani ya Mavuto Ayankhidwa.
Kuphunzila Baibo kungakuthandizeni kupeza citonthozo tsoka likagwa.
Pezani Thandizo pa Nkhawa Zanu
Anthu ambili amavutika na nkhawa. Komabe, pali zambili zimene mungacite kuti mupeze thandizo lofunikila.
Thandizo kwa Acinyamata
Onani mmene Baibo ingathandizile acinyamata pa mavuto amene amakumana nawo nthawi zambili.