N’ciani Catsopano?
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
Ndimakondwera Kuchita Chifuniro Chanu (Nyimbo ya Msonkhano Wachigawo wa 2025)
Tikamatengera chitsanzo cha Yesu cha kukhala omvera, nafenso timapeza chimwemwe pochita chifuniro cha Mulungu.
NYIMBO ZOPEKEDWA KOYAMBA
Cifunilo Cake Cidzacitika Posacedwa
Posacedwapa tidzasangalala ndi madalitso m’dziko latsopano.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Kukumbukila Malemba
Pezani mfundo zitatu zimene zingakuthandizeni kukumbukila malemba.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
Mlangizi Wathu Wamkulu Watiphunzitsa kwa Moyo Wathu Wonse
Franco Dagostini wacitako mautumiki osiyanasiyana, waphunzila zikhalidwe zosiyanasiyana ndipo waphunzilanso zilankhulo zosiyanasiyana. Iye akufotokoza maphunzilo ofunika amene waphunzila kwa Mlangizi Wamkulu, Yehova.
NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA
June 2025
Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila kuyambila August 18–September 14, 2025.
UMOYO NA UTUMIKI WATHU–KABUKU KA MISONKHANO
July–August 2025
PHUNZILANI KWA MABWENZI A YEHOVA—ZOCITA
Abigayeli
Mungaphunzile ciyani kwa Abigayeli amene anali bwenzi la Yehova?
MABUKU NA MABULOSHA