Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Trinidad and Tobago
The Assn of JWs of Trinidad and Tobago
Lower Rapsey St and Laxmi Lane
CUREPE
TRINIDAD AND TOBAGO
+1 868-663-3392
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Mphindi. 45
Zimene Timacita
Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’dziko la Trinidad ndi Tobago, ndiponso ku Guyana.