Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Peru
Jirón El Cortijo 329
Monterrico Chico. Santiago de Surco
LIMA 33
PERU
+51 1-434-1474
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs
Nthawi yoona malo: Ola limodzi
Zimene Timacita
Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cikwecuwa (ca ku Ancash), Cikwecuwa (ca ku Ayacucho), Cikwecuwa (ca ku Cuzco), Cishipibo-konibo, Ciawajuni, ndi cinenelo ca manja ca ku Peru.