Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Netherlands

Christelijke Gemeente van Jehovah’s Getuigen in Nederland

Noordbargerstraat 77

7812 AA EMMEN

NETHERLANDS

+31 591-683555

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:00hrs mpaka 15:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi

Zimene Timacita

Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cidaci. Timapanga zofalitsa za akhungu m’zinenelo 12. Timapanganso ma CD ndi mavidiyo a zofalitsa m’zinenelo zambili.

Tengani kapepala koonetsa malo.