Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Haiti
Santo 20, No. 9
Route de Croix-des-Bouquets
PORT-AU-PRINCE
HAITI
+509 2813-1560
+509 2813-1561
+509 2813-1562
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Ola limodzi
Zimene Timacita
Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cikiliyo ca ku Haiti ndiponso timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova m’mipingo yoposa 200 ya m’dzikoli.