Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Finland
Puutarhatie 60
FI-01300 VANTAA
FINLAND
+358 9-825-885
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
8:00hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:30 mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu
Zimene Timacita
Ofesiyi imayang’anila nchito ya Mboni za Yehova pafupifupi 29,000 za m’dzikoli, za ku Estonia, Latvia, ndi ku Lithuania. Imayang’anilanso nchito yomasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’zinenelo 6 ndi m’zinenelo zinai za manja.