Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
Chile
Ave Concha y Toro 3456
PUENTE ALTO
CHILE
+56 2-428-2600
+56 2-428-2609 (Fax)
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
9:00hrs mpaka 10:30hrs ndi 13:30hrs mpaka 15:00hrs
Nthawi yoona malo: Ola limodzi
Zimene Timacita
Timayang’anila nchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu Baibulo m’dzikoli. Timatumiza mabuku kumipingo yoposa 800.