Funa Moyo Wamuyaya
Daunilodi:
1. M’dzikoli zimavuta
kusatsatila mtima na kucita zoyenela.
(MWANA WA KOLASI)
M’lungu amatiuza kuti tisatengele dziko
Atilonjeza Paradaiso.
(KOLASI)
Usagwe, pilila
Yehova ali nawe sadzakusiya
Ndipo pemphela
kuti akuthandize uzipilila
Ganizila zinthu za kutsogolo.
2. Angafune uchuke
Kuti dzina lako lizimveka kulikonse
(MWANA WA KOLASI)
Koma ni zopanda pake
Tumikilabe Yehova
Akulonjeza Paradaiso.
(KOLASI)
Usagwe, pilila
Yehova ali nawe sadzakusiya
Ndipo pemphela
kuti akuthandize uzipilila.
Ganizila zinthu za kutsogolo.
(KOLASI)
Usagwe, pilila
Yehova ali nawe sadzakusiya
Ndipo pemphela
kuti akuthandize uzipilila.
Ganizila zinthu za kutsogolo.