Nkhani ya Yona—Kutengapo Phunzilo pa Kulimba Mtima na Cifundo
Mneneli Yona anayamba wakana kulabadila mawu a Yehova akuti akalalikile za ciweluzo ku mzinda wa Nineve, ku Asuri; koma cifukwa ca zocitika zoopsa zotsatilapo, iye anaphunzila tanthauzo leni-leni la kulimba mtima na cifundo.
Mungakondenso Izi
KUŴELENGA BAIBO MONGA SEŴELO