NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA December 2016

Magaziniyi ili na nkhani zophunzila m’mlungu wa January 30 mpaka February 26, 2017.

MBILI YANGA

Kukhala “Zinthu Zonse Kwa Anthu Osiyana-siyana”

Maudindo ambili amene Denton Hopkinson anali nawo kwa zaka zambili anamuthandiza kuona mmene Yehova amakondela anthu a mitundu yonse.

Tinamasulidwa mwa Cisomo ca Mulungu

Mudzapindula kwambili mukaganizila mmene Yehova anakumasulilani ku ucimo

‘Kuika Maganizo Athu pa Zinthu za Mzimu Kumabweletsa Moyo na Mtendele’

Aroma caputa 8 ili na malangizo amene angakuthandizeni kukalandila mphoto imene Yehova analonjeza mtundu wa anthu.

Kodi Mukumbukila?

Kodi mwaŵelenga mosamala magazini aposacedwapa a Nsanja ya Mlonda? Onani kuti ni mafunso angati ozikidwa pa Baibo amene mungakwanitse kuyankha.

Tulilani Yehova Nkhawa Zanu Zonse

Nthawi zina, atumiki a Mulungu amakhala na nkhawa. Onani njila zinayi zimene zingakuthandizeni kupindula na “mtendele wa Mulungu.”

Yehova Amapeleka Mphoto kwa Anthu Omufuna-funa na Mtima Wonse

Kodi ciyembekezo codzalandila mphoto kwa Yehova cimatipindulitsa bwanji? Kodi anawadalitsa bwanji atumiki ake akale? Nanga masiku ano amawadalitsa bwanji atumiki ake?

Kufatsa​—Kumaonetsa Nzelu

Si capafupi kukhalabe wofatsa tikacitilidwa zinthu mopanda cilungamo, koma Baibo imalimbikitsa Akhiristu kukhala ofatsa. N’ciani cingakuthandizeni kukhala na khalidwe laumulungu limeneli?

Mlongoza Nkhani wa Nsanja ya Mlonda 2016

Mndandanda wa nkhani zofalitsidwa mu Nsanja ya Mlonda yogaŵila na yophunzila.