Onani zimene zilipo

Magazini a Nsanja ya Mlonda na Galamuka!

Magazini athu amenewa a nkhani zozikidwa pa Baibo mugawacite daunilodi mu vitundu mahadiledi, kuphatikizapo vitundu va manja. Nsanja ya Mlonda imatiunikila tanthauzo la zocitika zikulu-zikulu za padziko mogwilizana na maulosi a m’Baibo. Imatonthoza anthu powapatsa uthenga wabwino wokamba za Ufumu wa Mulungu, ndiponso imalimbikitsa cikhulupililo mwa Yesu Khristu. Magazini ya Galamuka! imatithandiza mmene tingacitile na mavuto a masiku ano. Imatipatsanso cidalilo m’lonjezo la Mlengi wathu la dziko latsopano la bata na mtendele.

Sankhani citundu pa danga la citundu, ndipo tinikani pakuti Fufuzani kuti muone magazini na mipangidwe yake m’citunduco.

 

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

January 2025

Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila mu mlungu wa March 3–​April 6, 2025.

GALAMUKA!

Mungadziteteze Bwanji ku Mavuto a m’Dzikoli?

Nkhani za m’magazini ino zili na mfundo zimene zingathandize inu na okondedwa anu kuti musamakhudzidwe kwambili na zocitika za m’dzikoli zimene zikuipilaipila.

ONANI

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

GALAMUKA!

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA

NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA