Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Mmene Kabuku aka Kangakuthandizileni

Mmene Kabuku aka Kangakuthandizileni

Kabuku aka kadzakuthandizani kukhala ndi mtima wokonda kuphunzila Mau a Mulungu, Baibo. Malemba amene ali kumapeto kwa palagalafu iliyonse aonetsa kumene mungapeze mayankho m’Baibo yanu pa mafunso amene ali m’zilembo zakuda kwambili.

Pamene muŵelenga Malemba, muziona mmene malembawo ayankhila mafunso amenewa. Aliyense wa Mboni za Yehova ni wokonzeka kukuthandizani kuti mumvetsetse tanthauzo la Malembawo.​—Ŵelengani Luka 24:32, 45.

Cidziŵitso: Mabuku onse amene achulidwa m’kabuku aka ni olembedwa ndi Mboni za Yehova.