Pulogilamu ya Msonkhano wa Dela wa 2017-2018—Wa Woyang’anila Dela
Onani pulogilamu ya msonkhano wa delawu, umene uli na nkhani zitatu za woyang’anila dela
Musaleme pa Kucita Zabwino!
N’cifukwa ninji kucita zabwino kumakhala kovuta, koma n’ciani cingatithandize?
Pezani Mayankho pa Mafunso Aya
Mafunso aya adzayankhiwa pa msonkhanowu