Ziŵelengelo Zonse za mu 2023
Nthambi za Mboni za Yehova: 85
Ciŵelengelo ca Maiko Ocitila Lipoti: 239
Ciŵelengelo ca Mipingo Yonse: 118,177
Opezeka pa Cikumbutso Padziko Lonse: 20,461,767
Amene Anadya Ziphiphilitso Padziko Lonse: 22,312
Ofalitsa a Onse Amene Anagwila Nchito Yolalikila: 8,816,562
Avaleji ya Ofalitsa Amene Anali Kulalikila Mwezi Uliwonse: 8,625,042
Kuwonjezeka kwa Ofalitsa Kucokela mu 2022: 1.3
Onse Amene Anabatizika b: 269,517
Avaleji ya Apainiya c Mwezi Uliwonse: 1,570,906
Avaleji ya Apainiya Othandiza Mwezi Uliwonse: 738,457
Maola Onse Amene Tinathela mu Utumiki: 1,791,490,713
Avaleji ya Maphunzilo a Baibo d Mwezi Uliwonse: 7,281,212
Caka ca utumiki ca 2023 cinayamba pa September 1, 2022, ndipo cinatha pa August 31, 2023.
a Wofalitsa ni munthu amene amalalikila mwakhama uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu. (Mateyu 24:14) Kuti mudziŵe mmene timapezela ciŵelengeloci, onani nkhani yakuti “Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?” pa jw.org ku Chichewa.
b Kuti mudziŵe zimene mungacite kuti mubatizike n’kukhala wa Mboni za Yehova, onani nkhani yakuti “Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?” pa jw.org ku Chichewa.
c Mpainiya ni wa Mboni wacitsanzo cabwino amene amadzipeleka kuti azilalikila uthenga wabwino kwa maola ena ake mwezi uliwonse.
d Kuti mudziŵe zambili, onani nkhani ya pa jw.org yakuti, “Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?”