September 21-27
EKSODO 27-28
Nyimbo 25 na Pemphelo
Mau Oyamba (1 min.)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kodi Tingaphunzile Ciani pa Zovala za Ansembe?”: (10 min.)
Eks. 28:30—Tifunika kufuna-funa citsogozo ca Yehova (it-2 1143)
Eks. 28:36—Tifunika kukhalabe oyela (it-1 849 ¶3)
Eks. 28:42, 43—Tifunika kucita zinthu mwaulemu polambila Yehova (w08 8/15 15 ¶17)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)
Eks. 28:15-21—Kodi miyala yamtengo wapatali imene inali kuikidwa pacovala pacifuwa ca mkulu wa ansembe ku Isiraeli anali kuitenga kuti? (w12 8/1 26 ¶1-3)
Eks. 28:38—Kodi “zinthu zopatulika” zinali ciani? (it-1 1130 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Eks. 27:1-21 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kakhadi kongela pa jw.org. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi Yathu. (th phunzilo 2)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lvs 111 ¶20-21 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Anthu Amene Sanatuluke m’Nyumba”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani na kukambilana vidiyo yoyamba, ndiyeno tambitsani na kukambilana vidiyo yaciŵili.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) jy mutu 133
Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)
Nyimbo 46 na Pemphelo