Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 1-2

Zimene Zimabweletsa Macimo na Imfa

Zimene Zimabweletsa Macimo na Imfa

1:14, 15

Ngati mwayamba kuganizila zinthu zolakwika, citani izi:

  • Yambani kuganizila zinthu zina zabwino.—Afil. 4:8

  • Ganizilani mavuto amene mungakumane nawo ngati mwagonja ku ciyeselo.—Deut. 32:29

  • Pemphelani.—Mat. 26:41

izila zinthu zolakwika, ni zinthu zolimbikitsa ziti zimene mungaganizile m’malomwake?