Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

September 25–October 1

DANIELI 4-6

September 25–October 1
  • Nyimbo 67 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kodi Mukutumikila Yehova Mosalekeza?”: (10 min.)

    • Dan. 6:7-10—Danieli anaika moyo wake paciswe pofuna kutumikila Yehova mosalekeza (w10 11/15 peji 6 pala. 16; w06 11/1 peji 24 pala. 12

    • Dan. 6:16, 20—Mfumu Dariyo inaona kuti Danieli anali paubwenzi wolimba na Yehova (w03 9/15 peji 15 pala. 2

    • Dan. 6:22, 23—Yehova anadalitsa Danieli cifukwa cosagwedezeka pakumulambila (w10 2/15 peji 18 pala. 15)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Dan. 4:10, 11, 20-22—Kodi mtengo waukulu umene Nebukadinezara analota umaimila ciani? (w07 9/1 peji 18 pala. 5)

    • Dan. 5:17, 29—N’cifukwa ciani poyamba Danieli anakana mphatso zocokela kwa Mfumu Belisazara, koma pambuyo pake analandila? (w88 10/1 peji 30 mapa. 3-5; dp peji 109 pala. 22)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Dan. 4: 29-37

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) inv

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) inv—Citani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa kapepa ka ciitano kamene kanagaŵilidwa pa ulendo woyamba.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 129 pala. 16—Limbikitsani wophunzila kukhalabe wokhulupilika pamene akutsutsidwa ndi a m’banja lake.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU