September 11-17
EZEKIELI 46-48
Nyimbo 134 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Madalitso Amene Isiraeli Wobwezeletsedwa Anali Kudzalandila”: (10 min.)
Ezek. 47:1, 7-12—Nthaka inali kudzakhalanso yaconde (w99 3/1 peji 10 mapa. 11-12)
Ezek. 47:13, 14—Banja lililonse linali kudzalandila coloŵa cake (w99 3/1 peji 10 pala. 10)
Ezek. 48:9, 10—Asanagaŵile anthu malo, anali kupatulilatu “gawo” lina kuti likhale “copeleka” kwa Yehova
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Ezek. 47:1, 8; 48:30, 32-34—N’cifukwa ciani Ayuda a ku ukapolo sanayembekezele kuti zonse zokhudza masomphenya a Ezekieli a kacisi adzakwanilitsika mwakuthupi? (w99 3/1 peji 11 pala. 14)
Ezek. 47:6—N’cifukwa ciani Ezekieli akuchulidwa kuti “mwana wa munthu”? (it-2 peji 1001)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 48:13-22
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) wp17.5 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) wp17.5—Citani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa magazini imene inagaŵilidwa pa ulendo woyamba. Ndiyeno muonetseni imodzi mwa mabuku athu otsogozela phunzilo la Baibo.
Phunzilo la Baibo: (6 min. kapena kucepelapo) bhs peji 35 pala. 17—Muitanileni ku misonkhano.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Apo ayi, kambilanani zimene tiphunzilapo mu Buku Lapacaka. (yb17 peji 64-65)
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 17 mapa. 19-20, bokosi “Masukulu Ophunzitsa Atumiki a Ufumu,” na kabokosi kobwelelamo “Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 11 na Pemphelo