1 PETULO 1-2
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |“Mukhale Oyela”
1:14-16
Tiyenela kukhala oyela, kapena kuti aukhondo, kuti kulambila kwathu kukhale kovomelezeka kwa Yehova. Kodi kumatanthauzanji kukhala woyela . . .
-
mwauzimu?
-
m’makhalidwe?
-
mwakuthupi?