December 18-24
YOBU 28-29
Nyimbo 39 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mbili Yanu Ili Ngati ya Yobu?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yobu 29:24—Kodi tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca Yobu? (g00 7/8 11 ¶3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 28:1-28 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana naye mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 17)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 13, mawu oyamba pa cigawo cakuti Kumbani Mozamilapo na mfundo 4 (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Zimene Ningacite Kuti Niteteze Mbili Yabwino ya Gulu Lathu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) bt mutu 3 ¶12-18
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 50 na Pemphelo