Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

November 20-26

MIKA 1-7

November 20-26
  • Nyimbo 31 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Kodi Yehova Amafunanji kwa Ise?”: (10 min.)

    • [Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Mika.]

    • Mika 6:6, 7—Nsembe zathu zingakhale zopanda pake kwa Yehova ngati tilephela kucitila zabwino abale athu (w08 5/15 peji 6 pala. 20)

    • Mika 6:8—Zimene Yehova amafuna kwa ife zonse n’zotheka (w12 11/1 peji 22 pala. 4-7)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Mika 2:12—Kodi ulosiwu unakwanilitsika bwanji? (w07 11/1 peji 15 pala. 6)

    • Mika 7:7—N’cifukwa ciani tiyenela ‘kuyembekezela moleza mtima’ pa Yehova (w03 8/15 peji 24 pala. 20)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Mika 4:1-10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Sal. 83:18—Phunzitsani Coonadi. Yalani maziko a ulendo wobwelelako.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) Eks. 3:14—Phunzitsani Coonadi. Yalani maziko a ulendo wotsatila.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 132 mapa. 20-21.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU