June 27–July 3
2 SAMUELI 15-17
Nyimbo 123 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 16:4—Tingaphunzilepo ciyani pa cigamulo cimene Davide anapanga mosaganizila bwino? (w18.08 6 ¶11)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 17:17-29 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 7)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 2)
Nkhani: (Mph. 5) w09 5/15 27-28—Mutu: Tengelani Citsanzo ca Kukangalika kwa Itai pa Utumiki Wanu.—2 Sam. 15:19-22 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
“Cikondi . . . Sicidzikuza”: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili—Sicidzikuza.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 10
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 87 na Pemphelo