Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”

“Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”

Muzimvela Yehova cifukwa comuopa na kum’konda (Deut. 10:12; w09 10/1 10 ¶3-4)

Kumvela kumabweletsa madalitso (Deut. 10:13; w09 10/1 10 ¶6)

Yehova amafuna kuti tikhale bwenzi lake (Deut. 10:15; cl 16 ¶2)

Yehova satikakamiza kuti tizimumvela. Koma amafuna kuti tizimukonda na kumumvela “mocokela pansi pamtima.” (Aroma 6:17) Anthu amene asankha kutumikila Yehova amakhala na umoyo wabwino koposa.