Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 38-39

Yehova Sanamusiye Yosefe

Yehova Sanamusiye Yosefe

39:1, 12-14, 20-23

Pa nthawi imene Yosefe anakumana na mayeselo ambili, Yehova anali kudalitsa “ciliconse cimene iye anali kucita.” Ndipo “anacititsa mkulu wa ndende kum’konda.” (Gen. 39:2, 3, 21-23) Kodi tiphunzilapo ciani pa nkhaniyi?

  • Mayeselo amene timakumana nawo si umboni wakuti Yehova sakondwela nafe.—Sal. 34:19

  • Tifunika kuona mmene Yehova akutidalitsila na kukhala woyamikila.—Afil. 4:6, 7

  • Tifunika kudalila Yehova kuti atithandize. —Sal. 55:22