March 13-19
1 MBIRI 27-29
Nyimbo 133 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tate Apeleka Uphungu Wacikondi kwa Mwana Wake”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Mbiri 27:33—Kodi Husai anaonetsa bwanji kuti ni citsanzo cabwino pa nkhani yokhala bwenzi lokhulupilika? (w17.03 29 ¶6-7)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 27:1-15 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Yesu—Mat. 20:28. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso ndipo anaonetsa cidwi. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Yesu Anafa? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 9)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene analandila kapepala koitanila anthu ku Cikumbutso ndipo anaonetsa cidwi. Yambitsani phunzilo la Baibo m’bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya. (th phunzilo 6)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)
Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita: (Mph. 10) Onetsani vidiyo ya Zimene Gulu Lakwanitsa Kucita ya March.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 40
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 45 na Pemphelo