GENESIS 46-47
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU |Thandizo la Cakudya pa Nthawi ya Njala
47:13, 16, 19, 20, 23-25
Masiku ano, anthu m’dzikoli ali na njala yauzimu. (Amosi 8:11) Kupitila mwa Khristu Yesu, Yehova amapeleka cakudya cauzimu ca mwana alilenji.
-
Mabuku ophunzilila Baibo
-
Misonkhano ya mpingo
-
Misonkhano yadela komanso yacigawo
-
Zomvetsela
-
Mavidiyo
-
JW.ORG
-
JW Broadcasting
Kodi nimadzimana zinthu ziti kuti nizidya cakudya cauzimu pa tebulo la Yehova nthawi zonse?