Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

June 11-17

LUKA 1

June 11-17
  • Nyimbo 137 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • Tengelani Kudzicepetsa kwa Mariya”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Luka 1:69—Kodi mau akuti “nyanga yacipulumutso” atanthauza ciani? (“nyanga yacipulumutsonwtsty mfundo younikila)

    • Luka 1:76—Kodi Yohane M’batizi ‘anatsogola pamaso pa Yehova’ m’lingalilo lanji? (“udzatsogola pamaso pa Yehovanwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Luka 1:46-66

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 92

  • Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Ngati mufuna, kambilanani mfundo zokhudza lemba la caka ca 2018. (w18.01 mape. 8-9 mapa. 4-7)

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 24

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 58 na Pemphelo