June 12-18
MALIRO 1-5
Nyimbo 128 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Kuyembekezela Moleza Mtima Kumatithandiza Kupilila”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo ya Mfundo Zokhudza Buku la Maliro.]
Maliro 3:20, 21, 24—Yeremiya anayembekezela moleza mtima ndipo anadalila Yehova (w12 6/1 peji 14 mapa. 3-4; w11 9/15 peji 8 pala. 8)
Maliro 3:26, 27—Kupilila mayeselo kudzatithandiza kulimbana na zovuta zamtsogolo (w07 6/1 peji 11 mapa. 4-5)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Maliro 2:17—N’ciani cimene Yehova “ananena” cimene cinakwanilitsika cokhudza Yerusalemu? (w07 6/1 peji 9 pala. 4)
Maliro 5:7—Kodi Yehova amaimba anthu mlandu cifukwa ca zolakwa za makolo awo akale? (w07 6/1 peji 11 pala. 1)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Maliro 2:20–3:12
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) g17.3 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) g17.3 nkhani ya pacikuto—Itanilani mwininyumba kumisonkhano.
Nkhani: (6 mineti kapena kucepelapo) w11 9/15 9-10 ¶11-13—Mutu Wake: Yehova Ndi Colowa Canga.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (8 min.) Apo ayi, kambilanani “Kalata Yocokela ku Bungwe Lolamulila” mu Buku Lapacaka. (yb17 peji 2-5)
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (7 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June 2017.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 13 mapa. 33-34, na bokosi “Zipambano za Kukhoti Zimene Zinapititsa Patsogolo Nchito Yolalikila, ndi bokosi lobwelelamo “Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 100 na Pemphelo