CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la 1 Mafumu.]
Adoniya anacitilidwa cifundo pambuyo pokonza ciwembu cakuti akhale mfumu (1 Maf. 1:5, 52, 53; it-2 987 ¶4)
Adoniya sanaphunzilepo kanthu pa colakwa cake, ndipo analangidwa (1 Maf. 2:15-17, 22, 23; it-1 49)
Munthu wanzelu amaphunzilapo kanthu pa zolakwa zake. Koposa pamenepo, amaphunzilapo kanthu pa zolakwa za ena.—1 Akor. 10:11.