1 TIMOTEYO 1-3
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 1Kalamilani Nchito Yabwino
3:1, 13
Zimakhala bwino ngati abale ayamba kukalamila ali acicepele. Izi zimawapatsa mwayi wakuti aphunzitsidwe, na kuonetsa kuti ni oyenelela kulandila udindo wokhala mtumiki wothandiza akadzakula. (1 Tim. 3:10) Kodi m’bale angacite ciani kuti akalamile udindo? Angacite zimenezi mwa kukulitsa na kuonetsa makhalidwe otsatilawa:
-
Kudzipeleka pa nchito.—km 7/13 2-3 ¶2
-
Kukonda zinthu zauzimu.—km 7/13 3 ¶3
-
Kudalilika na kukhulupilika.—km 7/13 3 ¶4