January 1-7
YOBU 32-33
Nyimbo 102 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Tonthozani Omwe Ali na Nkhawa
(Mph. 10)
Khalani mabwenzi kwa ena (Yobu 33:1; it-1 710)
Khalani acifundo m’malo mowaweluza (Yobu 33:6, 7; w14 6/15 25 ¶8-10)
Monga Elihu anacitila, yambani mwamvetsela na kuganizilapo musanalakhule (Yobu 33:8-12, 17; w20.03 23 ¶17-18; onani cithunzi pacikuto)
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Yobu 33:25—Kodi vesiyi itithandiza bwanji kusamada nkhawa kwambili na maonekedwe athu tikayamba kukalamba? (w13 1/15 19 ¶10)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zomwe mungakonde kutigaŵilako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Yobu 32:1-22 (th phunzilo 12)
4. Kambilanani pa Zokhudza Munthuyo—Mmene Yesu Anacitila Zimenezi
(Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani VIDIYO yakuti kenako kambilanani lmd phunzilo 1 mfundo 1-2.
5. Kambilanani pa Zokhudza Munthuyo—Tengelani Yesu
(Mph. 8) Makambilano ozikika pa lmd phunzilo 1 mfundo 3-5 komanso mbali yakuti “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo 116
6. Zofunikila za Mpingo
(Mph. 15)
7. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 4 bokosi pa tsa. 30