January 28–February 3
MACHITIDWE 27-28
Nyimbo 129 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Paulo Apita ku Roma”: (10 min.)
Mac. 27:23, 24—Mngelo anauza Paulo kuti iye pamodzi na onse amene anali nawo pa ulendowu adzapulumuka ku cimphepo ca m’kuntho (bt peji 208 pala. 15)
Mac. 28:1, 2—Ngalawa imene Paulo anakwela inasweka pa cisumbu cochedwa melita (bt peji 209 pala. 18; peji 210 pala. 21)
Mac. 28:16, 17—Paulo anafika bwino ku Roma (bt peji 213 pala. 10)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mac. 27:9—Kodi “kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba macimo” kunali kutanthauza ciani?(“kusala kudya kwa tsiku la mwambo wophimba macimo” nwtsty mfundo younikila)
Mac. 28:11—N’ciani cocititsa cidwi na cizindikilo ca ngalawa? (“Ana Amapasa a Zeu” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 27:1-12 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Kubwelelako Kaciŵili: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 2)
Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) lv mape. 139-141 mapa. 16-17 (th phunzilo 3)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Paulo Anayamika Mulungu Ndipo Analimba Mtima”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti “Citsulo Cimanola Citsulo Cinzake”—Kambali Kake. Limbikitsani onse kuti akatambe vidiyo yonse.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 52
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 93 na Pemphelo