Makambilano Acitsanzo
●○○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti malangizo otithandiza kukhala na umoyo wacimwemwe?
Lemba: Sal. 1:1, 2
Ulalo: Kodi kukonda ndalama na cuma kungasokoneze bwanji cimwemwe cathu?
○●○ ULENDO WOBWELELAKO WOYAMBA
Funso: Kodi kukonda ndalama na cuma kungasokoneze bwanji cimwemwe cathu?
Lemba: 1 Tim. 6:9, 10
Ulalo: Ni mapindu ati amene timapeza tikakhala acimwemwe?
○○● ULENDO WOBWELELAKO WACIŴILI
Funso: Ni mapindu ati amene timapeza tikakhala acimwemwe?
Lemba: Miy. 17:22
Ulalo: Kodi banja lingakhale bwanji lacimwemwe ngakhale pokumana na mavuto?