December 11-17
ZEKARIYA 1-8
Nyimbo 26 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Adzagwila Covala ca Munthu Amene ndi Myuda”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Zekariya.]
Zek. 8:20-22—Anthu amitundu yonse akufuna-funa Yehova (w14 11/15 peji 27 pala. 14)
Zek. 8:23—Aja ali na ciyembekezo codzakhala padziko lapansi, amacilikiza otsalila odzozedwa mofunitsitsa (w16.01 peji 21 pala. 4; w09 2/15 peji 27 pala. 14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Zek. 5:6-11—Kodi tili na udindo wanji tikadziŵa za coipa? (w17.10 peji 25 pala. 18)
Zek. 6:1—Kodi mapili aŵili amkuwa aimila ciani? (w17.10 mape. 27-28 mapa. 7-8)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Zek. 8:14-23
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) g17.6 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) g17.6 Onetsani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa magazini imene inagaŵilidwa pa ulendo woyamba. Kenako, yalani maziko a ulendo wotsatila.
Phunzilo la Baibo: (6 min. olo kucepelapo) fg Phunzilo 5 mapa. 1-2.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kufikila Munthu Aliyense m’Gawo Lathu”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kulalikila “Mpaka Kumalekezelo a Dziko Lapansi”
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 22 mapa. 17-24, na bokosi lobwelelamo Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 139 na Pemphelo