August 12-18
TITO 1–FILIMONI
Nyimbo 99 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kuika Akulu”: (10 min.)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Tito.]
Tito 1:5-9—Oyang’anila madela amaika munthu kukhala mkulu ngati wakwanilitsa ziyenelezo za m’Malemba (w14 11/15 28-29)
[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Filimoni.]
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Tito 1:12—N’cifukwa ciani mawu a pa vesiyi sacilikiza kusankhana mitundu? (w89 5/15 31 ¶5)
Filim. 15, 16—N’cifukwa ciani Paulo sanapemphe Filimoni kuti amasule Onesimo? (w08 10/15 31 ¶4)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Tito 3:1-15 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)
Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti. (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Acinyamata—Khalani ‘Odzipeleka pa Nchito Zabwino’”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti, Acicepele Olemekeza Yehova.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 79
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 127 na Pemphelo