April 22-28
1 AKORINTO 14-16
Nyimbo 22 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu Adzakhala ‘Zinthu Zonse kwa Aliyense’” (10 min.)
1 Akor. 15:24, 25—Ufumu wa Mesiya udzawononga adani onse a Mulungu (w98 7/1 21 ¶10)
1 Akor. 15:26—Imfa idzawonongedwa (kr 237 ¶21)
1 Akor. 15:27, 28—Khristu adzapeleka Ufumu kwa Yehova (w12 9/15 12 ¶17)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
1 Akor. 14:34, 35—Kodi mtumwi Paulo analetsa akazi kulankhula? (w12 9/1 9, bokosi)
1 Akor. 15:53—Kodi mawu akuti kusafa na kusawonongeka atanthauza ciani? (it-1 1197-1198)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) 1 Akor. 14:20-40 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako Woyamba: (5 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 63
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 103 na Pemphelo