Onani zimene zilipo

Baibo ya pa Intaneti

Ŵelengani na kumvetsela Baibo pa intaneti, kapena citani daunilodi kwaulele zomvetsela kapena mavidiyo a m’cinenelo ca manja a Baibo. Baibo ya Cimasulilo ca Dziko Latsopano ni yolondola, ndiponso yosavuta kuŵelenga. Inafalitsidwa yathunthu, kapena mbali yake cabe, m’zinenelo zoposa 210. Ndipo makope amene apulintidwa ni oposa 240 miliyoni.

ONANI