Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

OCTOBER 28, 2016
ZATSOPANO

Pemphani Kudzera pa Intaneti Kuti Mudzaone Malo

Pemphani Kudzera pa Intaneti Kuti Mudzaone Malo

Tsopano mutha kupempha kudzera pa intaneti kuti mudzaone malo ku maofesi athu a ku United States ku New York. Maofesiwa akuphatikizapo likulu lathu lomwe lili ku Warwick, Likulu la Maphunziro la Watchtower lomwe lili ku Patterson komanso ofesi ya nthambi ya United States yomwe ili ku Wallkill.

Konzani zoti mudzaone malo athu ku United States.