Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Kabuku ka Msonkhano
M’kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu timapezamo ndandanda komanso nkhani zimene timaphunzira pamisonkhano ya mkati mwa wiki, zomwe zikuphatikizapo ndandanda yowerengera Baibulo wiki iliyonse. Msonkhanowu ndi waulere ndipo aliyense ndi wolandiridwa.

