Zatsopano pa JW.ORG

2026-04-07

NYIMBO ZA BROADCASTING

Mumatambasula Dzanja Lanu

Kodi kupatsa kwa Yehova kukuthandiza bwanji mlongo wachitsikana kukhala wosangalala akagawira ena zinthu?

2026-04-06

TIMAPEPALA NDI ZOITANIRA

2026 Convention Invitation

2026-04-06

NYIMBO ZA BROADCASTING

Tikusangalala Chifukwa Maso Athu Amaona (Nyimbo ya Msonkhano wa 2026)

Imvani mmene mawu a Yesu amabweretsera chimwemwe chomwe chimatithandiza kuchepetsa nkhawa ndi kulimbitsa chiyembekezo chathu.

2026-04-06

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Kusindikiza Mabuku pa Nthawi Imene Zinthu Zathu Zambiri Zikupezeka pa Intaneti

Chifukwa chiyani tikufunika kupitirizabe kupulinta mabuku ndi zinthu zina?

2026-03-19

ZOCHITIKA PA MOYO

Anasintha Chifukwa Chophunzira Baibulo

Kodi M’bale Nguyễn anasitha bwanji kuchoka pa munthu wofunafuna ndalama n’kukhala munthu wosangalala? Kodi M’bale Phùng anasintha bwanji kuchoka pa moyo wokhala chigawenga n’kukhala ndi moyo wabwino?

2026-03-17

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Zinthu Zochititsa Chidwi za M’Baibulo​​—⁠Maukonde Otchulidwa M’Baibulo

Dziwani zambiri zokhudza maukonde otchulidwa m’Baibulo amene asodzi ankagwiritsa ntchito.

2026-03-17

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Mafunso Ochokera kwa Owerenga​​—⁠June 2026

Kodi Paulo ankanena za mapangano awiri ati pa Agalatiya 4:24?

2026-03-17

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndakhala Ndikutumikira Yehova ku Cuba kwa Zaka Pafupifupi 70

Gustavo Joseph akufotokoza mmene zinthu zinalili pa moyo wawo pa nthawi imene ankachita utumiki woyang’anira dera, ankalera ana komanso kutumikira pa Beteli.

2026-03-17

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

June 2026

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 10–​September 6, 2026.