Malo a Nkhani

 

Lipoti Lachiwiri la Bungwe Lolamulira la 2026

Mulipotili, timveketsa mmene tizionera nkhani yokhudza kugwiritsa ntchito magazi ako omwe posankha thandizo lachipatala komanso popangidwa opaleshoni.

2026-03-25

NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Lipoti Loyamba la Bungwe Lolamulira la 2026

Mulipotili, tikambirana malangizo atsopano omwe angatithandize kuti tizichititsa maphunziro a Baibulo ogwira mtima pogwiritsa ntchito buku la Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale.

A Mboni za Yehova Anamangidwa Chifukwa cha Zimene Amakhulupirira​​—Potengera Dera

Madera amene a Mboni za Yehova anamangidwa, ndipo nthawi zina amazunzidwa kwambiri, chifukwa cha zimene amakhulupirira ngakhale kuti umenewu ndi ufulu wawo.