SEPTEMBER 2, 2019
ZATSOPANO
Baibulo la Dziko Latsopano Latulutsidwa M’Chiluo
Pa 30 August, 2019, Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika linatulutsidwa m’chinenero cha Chiluo mumzinda wa Kisumu ku Kenya. Baibulo la Dziko Latsopano lamasuliridwa lathunthu kapena mbali zake zina m’zinenero 184.