NOVEMBER 19, 2021
ZATSOPANO
Buku la Maliko Layamba Kupezeka pa Intaneti
Panopa buku la Maliko lochokera mu Baibulo la Dziko Latsopano lokonzedwanso layamba kupezeka Mu Chinenero Chamanja cha ku Malawi ndipo laikidwa pa jw.org.