Cameroon
Ntchito Yomanga Ofesi ya Nthambi Yatsopano ku Cameroon Ili Mkati
Popeza kuti ntchito ya Ufumu ikupita patsogolo kwambiri ku Cameroon, a Mboni za Yehova akumanga ofesi ya nthambi yokulirapo ku Logbessou m’dera la Douala.