Mboni za Yehova Padziko Lonse

Saipan

Mfundo Zachidule—Saipan

  • 48,000—Chiwerengero cha anthu
  • 220—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 3—Mipingo
  • Pa anthu 224 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Micronesia

Anthu ochokera kumayiko ena amene akutumikira kuzilumba za m’nyanja ya Pacific zimenezi nthawi zambiri amakumana ndi mavuto atatu. Kodi amathana nawo bwanji?