Mfundo Zachidule—Tonga
- 104,000—Chiwerengero cha anthu
- 256—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 3—Mipingo
- Pa anthu 495 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Tinapeza ‘Ngale Yamtengo Wapatali’
Werengani nkhani ya moyo wosangalala wa a Winston ndi a Pamela Payne a ku Australia.